Add Explanation
Add Meaning
$album_name
$date_release
$writer_name
New! Read & write lyrics explanations
 • Highlight lyrics and explain them to earn Karma points.
Innocent P. Makuwira – Kwathu Sipadziko lyrics

Kwathu sipadziko ndingopitilira;
Ndazikundikira chuma kumwambako
Mngelo akodola pakhomo lammwamba
Ndipo dziko lapansi sindiyesa kwathu.
Mbuye ndinu bwenzi langa ndithu
Ndichitenji ngati kumwambako sikwathu
Mngelo akodola pakhomo lammwamba
Ndipo dziko lapansi sindiyesa kwathu.
Mayi watsogola muulemelero
Ndifuna kugwira dzanja lake, konko
Andiyembekeza chinthuchi ndidziwa
Ndipo dziko lapansi sindiyesa kwathuLyrics taken from http://www.lyricsmode.com/lyrics/i/innocent_p_makuwira/kwathu_sipadziko.html

 • Email
 • Correct

songmeanings

   Write about your feelings and thoughts

   Know what this song is about? Does it mean anything special hidden between the lines to you? Share your meaning with community, make it interesting and valuable. Make sure you've read our simple tips.
   U
   Min 50 words
   Not bad
   Good
   Awesome!

   Featuredlyrics

   Explain