Add Explanation
Add Meaning
$album_name
$date_release
$writer_name
New! Read & write lyrics explanations
 • Highlight lyrics and explain them to earn Karma points.
Langwan Piksy – Tsoka Liyenda lyrics

Kumbire adanka nawo
Palibe akanakhonza
Anasiya pa dzuwa anawo
Anayesa ndi malodza
Ankati satana
Wakhala pa nsana
Kuyamba kudana
Kufuna kuphana
Kuthana
Nzosauzana
Nthawi yakwana
Buluzi wa easy chitseko cha mpana

Chorus
Anapita ndi nyanga zomwe kumanda
Anapita ndi nyanga zomwe kumanda
Ayo
Tsoka Liyenda
Ayo
Tsoka Liyenda

Bambo awa anali chikhwaya
Ana moyo wawo sanamve kuwawa
Ku school akapita amathawa
Zinavuta ndi za nchere analawa
Yes
Sanauzidwe za moyo
Anapeza bwanji makolo
Chuma
Moyo unakoma
Opanda zo khoma
Kupeza izo afuna
Ohh dzi ana ulesi
Bambo awo atsamira nkono

Akuti zonsezi
Ndi curse
Chayabwa chitedze
Mavuto pang'ono see they stressed
Chorus
Anapita ndi nyanga zomwe kumanda
Anapita ndi nyanga zomwe kumanda
Ayo
Tsoka Liyenda
Ayo
Tsoka Liyenda

Mudziwaphunzitsa ana
Skupangira pa mawa
Asamayese ngati ophweka moyo
Mukadzapita adzakhala akapolo

Musama yiwale
Kuti zanu munapanga kale
Nzeru zanu sizingatsale
Mungadzavutitse abale
Mdzakolola zomwe mudzale
Chuma ichi sangasamale
Ngati panopa simuphunzitsa
Mapangidwe ake mukumpusitsa
Tsoka ilo
Chorus
Anapita ndi nyanga zomwe kumanda
Anapita ndi nyanga zomwe kumanda
Ayo
Tsoka Liyenda
Ayo
Tsoka LiyendaLyrics taken from http://www.lyricsmode.com/lyrics/l/langwan_piksy/tsoka_liyenda.html

 • Email
 • Correct
Submitted byLangwan_Piksy

songmeanings

   Write about your feelings and thoughts

   Know what this song is about? Does it mean anything special hidden between the lines to you? Share your meaning with community, make it interesting and valuable. Make sure you've read our simple tips.
   U
   Min 50 words
   Not bad
   Good
   Awesome!
   This page is missing some information about the song. Please expand it to include this information. You can help by uploading artist's image, adding song structure elements, writing song meaning or creating lyrics explanation.

   Featuredlyrics

   Explain