preview
CHORUS
Umandipatsa appetite
Ndiwe appetizer
Umandipatsa mphamvu zambiri
Ndiwe energizer
Umanditsitsa mtima
Ndiwe stabilizer
Umandipatsa appetite
Kantima kofuna kudya
Appettizer
|
|
preview
VERSE ONE – PIKSY
Mmudzi uwu anthu amandikonda kwambiri
Amfumu ati ndiime u MP
Ati nyimbo za ine ziri amazing
Pazokha zitha kukwana kukhala ngati incentive
Ku wina u MP no campaign
Opikisana nawo akuchita complain
Kuchipangitsa Chambo kufeela ngati Ncheni
And position yanga ndikuichitabe maintain
Mu nyimbomu, ndikondwera mmenemu
Bambo Nyimbo
|
|
preview
Kukumazizira kukada
Tsiku kuchedwa kutha kukacha
Tsiku lonse mvula mawawa
Sindingachedwe ndidziwe za mawa
Mano anga anthu sawaona
Sikweni kweni kusekelera
Usiku zindivuta kugona
Ngati udzudzu ndimachezera
Moyo wathu dzana unkakoma
Kachikondi kutsekemera
Kuzizira
|
|
preview
INTRO
Okay…intro kaye
Hmmm mmm hm hm hm hm
Koma ndikaponya beat
Ndingobwera ndi ma hit
Sikuti ndikukweza kamba mu mtengo…... ndeno...
Mhu
CHORUS *2
Koma ndikaponya beat (Ponya mwendo)
Ndingobwera ndi ma hit (Ponya mwendo)
Ponya Mwendo
|
|
preview
VERSE ONE
Kumata kumata ndi superglue
Uli duu
Kuutolatola mtima wanga pansi uli mbuu
Kumata ndi bostic
Mbali zonse kuchta stick
2getha wambawamba osamvetsa yako logic
Unali wanga driver
So loyal to me sunasamale nkhan zomwe unazimva
Kundimatilira maso ako pa future
Unamata
|
|
preview
Chi Piksy Chinfarner Chodziwiker Ndi Boumurr
CHORUS
Hey Uncle
Uncle Short-one
Mukuganizira zotani
Uncle Short-one
Kuno ngini yakuphonyani
Uncle Short-one
Ndikale lija munatchona inu
Uncle Short-one
Uncle Short One
|
|