Dosage lyrics by Eminent Boiz - original song full text. Official Dosage lyrics, 2024 version | LyricsMode.com
Request & respond explanations
  • Don't understand the meaning of the song?
  • Highlight lyrics and request an explanation.
  • Click on highlighted lyrics to explain.
Eminent Boiz – Dosage lyrics
Verse 1

Kungodzuka mawa mami kufuna. ntakuonaaa
Nkona ndimabwera kwanu kusanache utha kuona

Chomwe ndimafuna Mami wekha sukudziwa
Koma chomwe ndimafuna mami ndekha ndimadziwa

Ndimataya ntima koma iwe sunditola
Kukusowa sindingathe poti nthawi sindilora

Tidadyetsana chani fanzi ati imangodabwa
Tima yoh tikakuyesa. tokhaso. kumangodabwa

Unaonamo. Mpaka lero simmadziwa
Ndilibe kalikose orso UNIMA anandisiya

Dosage yanga ndiwe sindi funa kukumisa
Ena akuti overdose mu chikondi unandimiza

CHORUS(HOOK)

Iiineyooo
Kukhala opanda iwe sindigathe mami

Ndiwe doSage yanga

Umafunika nthawi yoyenerera
Without U sindimava bwino ineeeE

Ndiwe dossage yanga* X4

M'mawa masana madzulo ndiwe babie

Verse 2

Iweyo NDE kanyale sinkuthira madzi or manyowa
Zonse Unganena ndiku Mvera ngati Duwa

Ndilibe ntima mami ndiwe amene Nakupatsa
Ukatalikira ndimadanda ndekha ntangofatsa

Ndi. Dzafusira mbeta adzandirore kwanu komwe
Nsidzaopa kamulako ngati zamlomwe

Mawa masana Madzulo mami umafunikiraaa
Opanda iwe nditha kufa
Osamwinikila

Ati Chikondi pa chikondi imakhala nkhani ina
Nde Abatiya pa iweyo amapanga nkhani ina

Dosage yanga ndiwe sindi funa kukumisa
Ena akuti overdose mu chikondi unandimiza

BACK TO HOOK

Verse 3

Ati swagg imandivuta ndinakhoza mpaka fail
Kodi tizinchonchonana? kukhala samatero

Amanena zambiri anthuwa ndimawamva
Koma sindiwatengera amavutika muntima

Ineyo opanda iwe na moyo umavuta
Ndiwe wanga wanga lady
Pamaso pa chauta

Dosage yokwanira sindipanga overdose
Ndikapanda kukuona ndimathakugwetsa Nsozi

Pamavuto pa ntendere mami
Umafunikira
Opanda iwe nditha kufa
Osapenekera

Dosage yanga ndiwe sindi funa kukumisa
Ena akuti overdose muchikondi unandimiza
×



Lyrics taken from /lyrics/e/eminent_boiz/dosage.html

  • Email
  • Correct

Dosage meanings

Write about your feelings and thoughts about Dosage

Know what this song is about? Does it mean anything special hidden between the lines to you? Share your meaning with community, make it interesting and valuable. Make sure you've read our simple tips.
U
Min 50 words
Not bad
Good
Awesome!

Post meanings

U
Min 50 words
Not bad
Good
Awesome!

official video

0-9 A B C D E F G H I J K L M N O P Q R S T U V W X Y Z